Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp18 No. 3 tsamba 16
  • Kodi Mulungu Amamva Bwanji Akamakuonani Mukuvutika?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mulungu Amamva Bwanji Akamakuonani Mukuvutika?
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • TAGANIZIRANI ZIMENE BAIBULO LIMANENA
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2017
  • “Amakuderani Nkhawa”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
  • Mungathe Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2019
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2017
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)——2018
wp18 No. 3 tsamba 16
Anthu akufufuza zina ndi zina pamalo pamene panayaka moto

Kodi Mulungu Amamva Bwanji Akamakuonani Mukuvutika?

Anthu ena amaganiza kuti Mulungu sizimam’khudza akamaona anthu akuvutika ndipo ena amaganiza kuti saona n’komwe.

TAGANIZIRANI ZIMENE BAIBULO LIMANENA

  • Mulungu amaona komanso amakhudzidwa tikamavutika

    “Yehova anaona kuti kuipa kwa anthu kwachuluka padziko lapansi . . . ndipo zinam’pweteka kwambiri mumtima.”​—Genesis 6:5, 6.

  • Mulungu adzathetsa mavuto onse

    “Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso. Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo. Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi, ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.”​—Salimo 37:10, 11.

  • Mulungu amatifunira zabwino

    “‘Maganizo anga kwa inu ndikuwadziwa bwino. Ndikuganizira zokupatsani mtendere osati masoka, kuti mukhale ndi chiyembekezo chabwino ndiponso tsogolo labwino,’ watero Yehova. ‘Mudzaitanira pa ine komanso mudzabwera ndi kupemphera kwa ine ndipo ine ndidzakumvetserani.’”​—Yeremiya 29:11, 12.

    “Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.”​—Yakobo 4:8.

Kuti mudziwe zambiri zokhudza chifukwa chimene Mulungu walolera kuti anthu azivutika, werengani mutu 11 m’buku ili, Zimene Baibulo Limaphunzitsa lofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova.

Bukuli likupezekanso pa www.jw.org/ny

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena