Mbiri Yateokratiki
Cape Verde: Chiŵerengero chapamwamba cha ofalitsa 861 chinachitira lipoti m’November. Ofalitsa ampingo anachita avareji ya maola 13 muutumiki wakumunda, ndipo maphunziro a Baibulo 1,798 anachititsidwa.
Nepal: Panali 576 amene anafika pa Msonkhano Wachigawo wa “Chiphunzitso Chaumulungu” mu Kathmandu, wochitidwa pa November 18-21, 1993.