Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 January tsamba 8
  • Kuphunzitsa Anthu Pogwiritsa Ntchito Kabuku ka Uthenga Wabwino

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kuphunzitsa Anthu Pogwiritsa Ntchito Kabuku ka Uthenga Wabwino
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Tizigwiritsa Ntchito Kabuku ka Uthenga Wabwino Pophunzitsa Anthu
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Nkhani Zatsopano Zoyambitsira Maphunziro A Baibulo
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2010
  • Gwiritsani Ntchito Kabuku Kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Tizisonyeza Anthu Mmene Timaphunzirira Baibulo Pogwiritsa Ntchito Buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 January tsamba 8

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Kuphunzitsa Anthu Pogwiritsa Ntchito Kabuku ka Uthenga Wabwino

  1. Werengani funso limene lalembedwa m’zilembo zakuda kwambiri kuti mwininyumba aganizire kwambiri mfundo yaikulu.

  2. Werengani ndime yake.

  3. Werengani malemba akuda kwambiri ndipo funsani mafunso amene angathandize munthuyo kuti apeze yankho la funso lija pa ndimeyo.

  4. Ngati m’munsi mwa funsolo muli ndime inanso, bwerezani mfundo 2 ndi 3. Ngati pa jw.org/ny pali vidiyo yomwe ikugwirizana mafunsowo, muonetseni mwininyumbayo.

  5. Kuti mutsimikizire ngati mwininyumbayo wamvetsa mfundo yaikulu, mufunseni mafunso akuda kwambiri aja.

Phunziro 2 m’kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu!
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena