CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 5-7
Anasiya Kuchita Zimene Mulungu Ankafuna
Yeremiya anaulula molimba mtima machimo ndiponso chinyengo cha Aisiraeli
Aisiraeli ankaganiza kuti kachisi ali ndi mphamvu inayake yapadera yoti ingawateteze
Yehova anawauza kuti nsembe zimene ankapereka mwamwambo sizingachotse machimo awo
Dzifunseni kuti: Kodi ndingatani kuti ndizilambira Yehova mogwirizana ndi zimene amafuna osati mwamwambo chabe?
Yeremiya waima pachipata cha nyumba ya Yehova