CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 15-17
Kodi Mumakwaniritsa Zimene Mwalonjeza?
Kodi Mfumu Zedekiya inaswa pangano lotani?
Kodi inakumana ndi zotani chifukwa cha kuswa panganoli?
Kodi ineyo ndinapanga malonjezo otani?
Kodi ndi zinthu ziti zimene zingachitike ngati nditaswa malonjezowa?