CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MATEYU 24
Pitirizani Kukhala Maso M’masiku Otsiriza Ano
Anthu ambiri masiku ano amalola kuti zinthu zatsiku ndi tsiku ziwalepheretse kuchita zinthu zokhudza kulambira. Kodi Akhristu olimba mwauzimu amasiyana bwanji ndi anthu a m’dzikoli pa nkhani ya mmene amaonera . . .
maphunziro apamwamba?
zosangalatsa?
ntchito?
chuma?