Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsamba 5
  • Anachiritsa Munthu pa Tsiku la Sabata

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anachiritsa Munthu pa Tsiku la Sabata
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Malamulo Ankalola Munthu Kuchita Chiyani pa Sabata?
    Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
  • Kodi Chololeka Nchiyani pa Sabata?
    Munthu Wamkulu Woposa Onse Amene Anakhalako
  • Kodi Nchiyani Chimene Chiri Chololedwa pa Sabata?
    Nsanja ya Olonda—1987
  • Kodi Akhristu Ayenera Kusunga Sabata?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 April tsamba 5
Munthu wolumala dzanja wafika kwa Yesu

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALIKO 3-4

Anachiritsa Munthu pa Tsiku la Sabata

3:1-5

N’chifukwa chiyani Yesu anakhumudwa ndi khalidwe la atsogoleri achipembedzo achiyuda? Iwo anachititsa kuti tsiku la Sabata likhale lolemetsa chifukwa cha malamulo ambirimbiri osafunika omwe anakhazikitsa. Mwachitsanzo, kupha ntchentche pa tsiku la Sabata linali tchimo. Kuchiritsa kunkakhala kovomerezeka pokhapokha ngati moyo wa munthu uli pangozi. Zimenezi zikutanthauza kuti munthu amene wathyoka fupa kapena kubinya samayenera kuthandizidwa pa tsiku la Sabata. Apa zikuonekeratu kuti atsogoleriwa sankaganizira munthu wolumala dzanja amene Yesu anam’chiritsa.

DZIFUNSENI KUTI:

  • ‘Kodi anthu ena amaona kuti ndine munthu wokakamira pa malamulo kapena amaona kuti ndine wachifundo?’

  • ‘Kodi ndingatsanzire bwanji Yesu pa nkhani yosonyeza chifundo ngati wina mumpingo wathu akufunika thandizo?’

Akulu awiri akuchita ulendo waubusa kwa mlongo yemwe amakhala wotanganidwa limodzi ndi mwana wake
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena