CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 2-3
Ananu, Kodi Mukuyesetsa Kuti Yehova Akhale Mnzanu Wapamtima?
Kuyambira ali mwana, Yesu anapereka chitsanzo chabwino pa nkhani yochita zimene Yehova amafuna komanso kulemekeza makolo ake.
Ananu, kodi mungatsanzire bwanji Yesu m’njira zotsatirazi?