Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 July tsamba 5
  • Yesetsani Kuti Mukhale Oyang’anira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesetsani Kuti Mukhale Oyang’anira
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Abale Achinyamata, Kodi Mukuyesetsa Kuti Muyenerere Udindo mu Mpingo?
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2013
  • N’chifukwa Chiyani Akhristu Akufunika Kuyesetsa Kuti Akhale Ndi Zolinga?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Ananu, Kodi Mukuyesetsa Kuti Yehova Akhale Mnzanu Wapamtima?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Atumiki Othandiza Amagwira Ntchito Yofunika Kwambiri
    Gulu Lochita Chifuniro cha Mulungu
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 July tsamba 5
M’bale wachinyamata akuyendetsa maikolofoni kumisonkhano, akuphunzira payekha komanso akuyendetsa mlongo wachikulire yemwe wakhala panjinga ya olumala

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 TIMOTEYO 1-3

Yesetsani Kuti Mukhale Oyang’anira

3:1, 13

Zimakhala bwino kwambiri abale akayamba kuchita zambiri mumpingo adakali aang’ono. Zimenezi zimawapatsa mpata woti asonyeze kuti ndi woyenerera kudzakhala atumiki othandiza akadzakula. (1 Tim. 3:10) Kodi m’bale angatani kuti akhale ndi udindo mumpingo? Ayenera kuyesetsa kumachita zinthu zotsatirazi:

  • Kudzipereka.​—km 7/13 2-3 ¶2

  • Kukonda zinthu zauzimu.​—km 7/13 3 ¶3

  • Kukhala wodalirika komanso wokhulupirika.—km 7/13 3 ¶4

Mkulu akuyankhula ndi wachinyamata yemwe akumuphunzitsa ntchito zina mumpingo
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena