Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsamba 7
  • Yehova Amakonda Munthu Wopereka Mokondwera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Amakonda Munthu Wopereka Mokondwera
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • ‘Timakobidi Tiwiri Tating’ono’ Tamtengo Wapatali
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • “Muzipereka Mphatso kwa Yehova”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Kodi Ndalama Zoyendetsera Ntchito ya a Mboni za Yehova Zimachokera Kuti?
    Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri
  • Yehova Amakonda Opatsa Mokondwerera
    Nsanja ya Olonda—1992
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 November tsamba 7
Mlongo wanyamula foni

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Yehova Amakonda Munthu Wopereka Mokondwera

Lemba la 2 Akorinto 9:7, limati: “Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika kapena mokakamizika, chifukwa Mulungu amakonda munthu wopereka mokondwera.” Masiku ano tili ndi njira zosavuta zomwe tingaperekere zopereka zathu. Mwachitsanzo, tikhoza kupereka kudzera pa intaneti pofuna kuthandiza pa ntchito zagulu lathu. Ntchitozi zingakhale zimene zikuchitika m’dziko lanu kapena padziko lonse.

ONERANI VIDIYO YAKUTI MMENE MUNGAPEREKERE ZOPEREKA PA ZIPANGIZO ZA MAKONO, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Patabuleti komanso pafoni patsegulidwa jw.org

    Kodi tingadziwe bwanji njira zina zomwe zili m’dziko lathu zokhudza mmene tingaperekere ndalama kudzera pazipangizo zamakono?

  • Banja likukambirana zokhudza ndalama zomwe angapereke

    Kodi anthu ena apindula bwanji chifukwa chopereka zopereka zawo kudzera pazipangizo zamakono?

  • Zizindikiro za njira zomwe tingaperekere ndalama zathu

    Kodi pali njira zinanso ziti zomwe tingaperekere zopereka zathu?

  • M’bale wachinyamata akuthandiza m’bale wachikulire kudziwa mmene angaperekere ndalama kudzera pa intaneti

    Kodi tingatani ngati sitikudziwa mmene tingagwiritsire ntchito zipangizo zamakonozi tikafuna kupereka zopereka zathu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena