Abulahamu akuphunzitsa Isaki zokhudza Yehova
Zimene Tinganene
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingadziwe bwanji zinthu zomwe zidzachitike m’tsogolo?
Lemba: Yes. 46:10
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi ndi maulosi a m’Baibulo ati amene akukwaniritsidwa masiku ano?
○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
Funso: Kodi ndi maulosi a m’Baibulo ati amene akukwaniritsidwa masiku ano?
Lemba: 2 Tim. 3:1-5
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi anthu adzasangalala ndi madalitso ati m’dziko limene Mulungu walonjeza?
○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
Funso: Kodi anthu adzasangalala ndi madalitso ati m’dziko limene Mulungu walonjeza?
Lemba: Yes. 65:21-23
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Yesu ali ndi udindo wotani pokwaniritsa zimene Mulungu analonjeza?