Nowa ndi banja lake akukonzekera kulowa m’chingalawa
Zimene Tinganene
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu dzina lake ndi ndani?
Lemba: Sal. 83:18
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi khalidwe lalikulu la Mulungu ndi chiyani?
○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
Funso: Kodi khalidwe lalikulu la Mulungu ndi chiyani?
Lemba: 1 Yoh. 4:8
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi munthu angatani kuti akhale bwenzi la Mulungu?
○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
Funso: Kodi munthu angatani kuti akhale bwenzi la Mulungu?
Lemba: Yoh. 17:3
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Yehova amatithandiza bwanji kudziwa zomwe zidzachitike m’tsogolo?