January 6-12
GENESIS 1-2
Nyimbo Na. 11 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Analenga Zamoyo Padziko Lapansi”: (10 min.)
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Genesis.]
Gen. 1:3, 4, 6, 9, 11—Zimene Mulungu analenga pa tsiku loyamba mpaka lachitatu (it-1 527-528)
Gen. 1:14, 20, 24, 27—Zimene Mulungu analenga pa tsiku la 4 mpaka la 6 (it-1 528 ¶5-8)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Gen. 1:1-19 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kusonyeza Kuti Nkhaniyo Ndi Yothandiza, kenako kambiranani phunziro 13 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w08 2/1 5—Mutu: Timakhala ndi Mtendere Wamumtima Tikazindikira Kuti Tinachita Kulengedwa. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Dokotala Woona za Mafupa Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake komanso yakuti, Katswiri Woona za Zinthu Zamoyo Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 67
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 78 ndi Pemphero