Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsamba 5
  • Yakobo Analandira Madalitso

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yakobo Analandira Madalitso
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Yakobo ndi Esau Akhululukirana
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Amapasa Amene Anali Osiyana
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Yakobo Analandira Madalitso
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 March tsamba 5
Yakobo wavala zovala za Esau komanso waika chikopa cha mbuzi m’khosi ndi m’mikono yake ndipo Isaki akukhudza mikono yake.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 27-28

Yakobo Analandira Madalitso

27:6-10, 18, 19, 27-29

Madalitso amene Yakobo analandira kuchokera kwa bambo ake, anali ulosi wa zimene zidzachitike m’tsogolo.

  • Mapu a Dziko Lolonjezedwa akusonyeza dera la Isiraeli lomwe ndi lobiriwira komanso lachonde mosiyana ndi dera la Edomu lomwe ndi louma kwambiri.

    27:28​—Yehova anapatsa mbadwa za Yakobo dziko lachonde “loyenda mkaka ndi uchi.”​—De 26:15

  • 27:29​—Aisiraeli (mbadwa za Yakobo) anadzakhala mtundu wamphamvu kuposa Aedomu (mbadwa za Esau).​—Ge 25:23; 2Sa 8:14

  • 27:29​—Aedomu anatembereredwa chifukwa ankadana ndi Aisiraeli ndipo patapita nthawi anawonongedwa.​—Eze 25:12-14

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena