Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 July tsamba 8
  • Muzidzichepetsa​—Muzipewa Kudzitama

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzidzichepetsa​—Muzipewa Kudzitama
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mumatsatira Yehova ndi Mtima Wonse?
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Achimwemwe Ali Odzichepetsa
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Muzitumikira Yehova Ndi Mtima Wonse
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Anthu 12 Anapita Kukaona Dziko la Kanani
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 July tsamba 8

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzidzichepetsa​—Muzipewa Kudzitama

Munthu akamadzitama amasonyeza kuti ndi wonyada, ndipo zimenezi sizilimbikitsa anthu ena. Choncho Baibulo limati: “Mlendo akutamande, osati pakamwa pako.”​—Miy 27:2.

ONERANI VIDIYO YAKUTI KHALANI BWENZI LA YEHOVA​—UZIDZICHEPETSA, NDIPO KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi ndi zinthu ziti zimene anthu amadzitama nazo?

  • N’chifukwa chiyani Kalebe amadzitama kwa mnzake?

  • Kodi bambo ake anamuthandiza bwanji kuti azidzichepetsa?

  • Kodi lemba la 1 Petulo 5:5 lingatithandize bwanji kukhala odzichepetsa?

Kalebe ali pamwamba ndipo akudzitamandira pamaso pa mnzake yemwe ali pansi.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena