Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsamba 2
  • Tizikonda Yehova Kuposa Mmene Timakondera Achibale Athu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tizikonda Yehova Kuposa Mmene Timakondera Achibale Athu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Mmene Tiyenera Kuchitira ndi Munthu Wochotsedwa
    Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’?
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Khalani Wokhulupirika ku Chikristu Wachibale Akachotsedwa mu Mpingo
    Utumiki wathu wa Ufumu—2002
  • Munthu Amene Mumamukonda Akasiya Kutumikira Yehova
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 December tsamba 2
Aroni Mkulu Wansembe waima m’bwalo la chihema chopatulika. Asuweni ake awiri anyamula mitembo ya Nadabu ndi Abihu kupita nawo kunja kwa msasa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 10-11

Tizikonda Yehova Kuposa Mmene Timakondera Achibale Athu

10:1, 2, 4-7

Nadabu ndi Abihu anyamula zofukizira n’kuikamo moto ndi zofukiza.

Wachibale wathu akachotsedwa zingakhale zovuta kusonyeza kuti ndife okhulupirika kwa Yehova. Akhristu omwe achibale awo ndi ochotsedwa angaphunzire mfundo yofunika pa malangizo amene Yehova anapatsa Aroni. Tiyenera kukonda kwambiri Yehova kuposa mmene timakondera achibale athu osakhulupirika.

Kodi Akhristu amene amachita zinthu mogwirizana ndi malangizo a Yehova okhudza anthu ochotsedwa amapeza madalitso otani?​—1Ak 5:11; 2Yo 10, 11

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena