Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 2
  • Pitirizani Kukhala Ndi Makhalidwe Oyera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pitirizani Kukhala Ndi Makhalidwe Oyera
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Pitirizani Kusonyeza Kuti Mumakonda Kwambiri Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Zikondwerero Zomwe Zimatikhudza
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • Yehova Amafuna Kuti Anthu Ake Azikhala Osiyana ndi Ena
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 2
Bambo akuyang’ana kumbali chifukwa choipidwa ndi zimene zabwera pakompyuta yake ndipo akutseka kompyutayo.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pitirizani Kukhala Ndi Makhalidwe Oyera

Yehova amafuna kuti tizikhala osiyana ndi anthu a m’dzikoli (Le 18:3; w19.06 27 ¶10)

Yehova amadana ndi machimo monga kugonana kwa pachibale, kwa amuna kapena akazi okhaokha komanso kugonana ndi nyama (Le 18:​6, 22, 23; w17.02 20 ¶13)

Yehova adzawononga anthu onse amene amachita makhalidwe oipa (Le 18:​24, 25; Miy 2:22; w14 7/1 7 ¶2)

Satana safuna kuti tidzalowe m’dziko latsopano. Koma mfundo za Yehova zingatiteteze ku msampha uliwonse wa Satana.

Kodi tingamusonyeze bwanji Yehova kuti timadana ndi makhalidwe oipa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena