Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 13
  • Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri Mu Utumiki​—Muzifunsa Mafunso
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muziwafika Pamtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzilola Kuti Yehova Azikuthandizani Kudzera M’pemphero
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzithandiza Ophunzira Baibulo Kuti Asiye Makhalidwe Oipa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI | ZIMENE MUNGACHITE KUTI MUZISANGALALA KWAMBIRI MU UTUMIKI

Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu

Mawu a Mulungu ndi amphamvu. (Ahe 4:12) Amafika pamtima anthu, ngakhale amene sadziwa Mulungu. (1At 1:9; 2:13) Timakhala ndi chimwemwe chodzadza tsaya tikaona munthu akusangalala ndi mfundo ya m’Baibulo yomwe tamusonyeza, imene kwa iyeyo ndi koyamba kuimva.

ONERANI VIDIYO YAKUTI MUZIWONJEZERA LUSO LANU KUTI MUZISANGALALA NDI NTCHITO YOPHUNZITSA​—MUZIGWIRITSA NTCHITO MAWU A MULUNGU NDIPO KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Chithunzi cha muvidiyo yakuti ‘Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala Ndi Ntchito Yophunzitsa​—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu.’ Anita akumvetsera pamene Jane akuwerenga lemba.

    Kodi Anita anagwiritsa ntchito bwanji Mawu a Mulungu pothandiza Jane kudziwa kuti ndi bwino kulola Mawu a Mulungu kuyankha mafunso athu?

  • Chithunzi cha muvidiyo yakuti ‘Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala Ndi Ntchito Yophunzitsa​—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu.’ Anita akumvetsera pamene Jane akuwerenga lemba mokweza.

    Kodi Anita anagwiritsa ntchito bwanji Mawu a Mulungu pouza Jane kuti awerenge lemba mokweza komanso potchula mfundo yaikulu ya lembalo?

  • Chithunzi cha muvidiyo yakuti ‘Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala Ndi Ntchito Yophunzitsa​—Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu.’ Jane akumumwetulira Anita.

    N’chiyani chikusonyeza kuti lemba lomwe linawerengedwa linamufika pamtima Jane, nanga mukuganiza kuti Anita anamva bwanji?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena