Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 4
  • Muzifunsira Nzeru kwa Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzifunsira Nzeru kwa Yehova
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • “Ine Ndine . . . Cholowa Chako”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kodi Makolo Angaphunzire Chiyani kwa Manowa ndi Mkazi Wake?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Samalani Kuti Musakhale Wonyada Ndi Wodzidalira
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzifunsira Nzeru kwa Yehova

Aisiraeli anapempha malangizo kwa Yehova mobwerezabwereza (Owe 20:17, 18, 23; w11 9/15 32 ¶2)

Aisiraeli anadalira kwambiri Yehova kuti awathandize kuyeretsa dzina lake (Owe 20:26-28)

Tiyenera kupitiriza kufufuza malangizo a Yehova n’kumamudalira kwambiri (Owe 20:35; Lu 11:9; w11 9/15 32 ¶4)

Zithunzi: 1. M’bale akuwerenga Baibulo komanso kufufuza m’mabuku athu. 2. M’bale uja akulankhula ndi dokotala wake ndipo akumusonyeza khadi lopereka malangizo a zachipatala.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Ndikakumana ndi mayesero, kodi nthawi yomweyo ndimapempha Yehova kuti andithandize? Kodi nthawi zonse ndimadalira Yehova kuti andipatse nzeru komanso anditsogolere?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena