Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsamba 4
  • “Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • “Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2016
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • Tizidzichepetsa Zinthu Zikatiyendera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 March tsamba 4
Goliyati yemwe ndi wamtali waima kumbuyo kwa womunyamulira chishango chake ndipo akunyoza Davide pamalo omenyera nkhondo.

Davide akufuna kumenyana ndi Goliyati

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”

Davide ankakhulupirira Yehova chifukwa cha zimene ankadziwa komanso anakumana nazo (1Sa 17:36, 37; wp16.5 11 ¶2-3)

Davide sankayerekezera Goliyati ndi iyeyo koma ankamuyerekezera ndi Yehova (1Sa 17:45-47; wp16.5 11-12)

Yehova anathandiza Davide kupambana pankhondo yolimbana ndi mdani amene anali wamphamvu kwambiri (1Sa 17:48-50; wp16.5 12 ¶4; onani chithunzi chapachikuto)

Bambo akutaya paketi ya ndudu motayamo zinyalala.

Nthawi zina tikhoza kukumana ndi mavuto akuluakulu, mwachitsanzo kuzunzidwa kapena kuvutika kusiya khalidwe loipa. Tikayamba kuona kuti mavutowo ndi aakulu, tizikumbukira kuti ndi aang’ono poyerekezera ndi mphamvu za Yehova.​—Yob 42:1, 2.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena