Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 8
  • Yehova Angakuthandizeni Kuti Mukwanitse Kuchita Utumiki Wovuta

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Angakuthandizeni Kuti Mukwanitse Kuchita Utumiki Wovuta
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Khalani Olimba Mtima Ngati Pinihasi
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Malangizo Achikondi a Bambo Opita kwa Mwana Wake
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Muzikhala Ndi Mantha Oyenera Poopa Kukhumudwitsa Yehova
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Muzithandiza Achinyamata Kuti Azichita Zambiri
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 8

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Angakuthandizeni Kuti Mukwanitse Kuchita Utumiki Wovuta

Alevi omwe anali alonda apachipata anali ndi udindo waukulu kwambiri (1Mb 9:26, 27; w05 10/1 9 ¶8)

Pinihasi anali mtsogoleri wa alonda a pachihema m’nthawi ya Mose (1Mb 9:17-20a)

Yehova anathandiza Pinihasi kukwaniritsa utumiki wake (1Mb 9:20b; w11 9/15 32 ¶7)

Zithunzi: 1. Mlongo wachinyamata akuyendetsa chithirakitala. 2. Banja lachikulire likuchita ulaliki wapafoni. 3. Banja likulalikira kumene kukufunika olalikira ufumu ambiri.

Yehova amatipatsa zochita zambiri zomwe zimakhala zofunika. Ngati simukudziwa bwino mmene mungachitire utumiki winawake, muzipemphera kwa Yehova komanso muzipempha Mkhristu wodziwa zambiri kuti akuthandizeni.​—Afi 2:13.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena