Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsamba 10
  • Muzikhala Wofunitsitsa Kuchita Zimene Mulungu Amafuna

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzikhala Wofunitsitsa Kuchita Zimene Mulungu Amafuna
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Davide ndi Sauli
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • “Kumvera Kuposa Nsembe”
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Chifukwa chake Davide Akuthawa
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Zimene Zili Mʼbuku la 1 Samueli
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 January tsamba 10
Zithunzi: 1. Modzikuza, Mfumu Sauli akupereka nsembe yopsereza paguwa lansembe. 2. Davide akukana kumwa madzi amene mmodzi mwa anyamata ake wamupatsa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzikhala Wofunitsitsa Kuchita Zimene Mulungu Amafuna

Sauli anali wosamvera, ndipo Yehova anamukana (1Mb 10:13, 14)

Yehova anasankha Davide kuti akhale mfumu m’malo mwa Sauli (1Mb 11:3)

Mosiyana ndi Sauli, Davide analola kuti malamulo komanso mfundo za Yehova zizimutsogolera (1Mb 11:15-19; w12 11/15 6 ¶12-13)

Davide ankakonda kuchita zimene Mulungu ankafuna. (Sl 40:8) Ifenso tingakhale ofunitsitsa kuchita zinthu zoyenera tikamaphunzira kuona zinthu mmene Yehova amazionera.—Sl 25:4; w18.06 17 ¶5-6.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena