Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsamba 7
  • “Yehova Akhoza Kukupatsani Zambiri Kuposa Pamenepa”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Yehova Akhoza Kukupatsani Zambiri Kuposa Pamenepa”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • “Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Ndi pa Nthawi Iti Pamene Tiyenera Kudalira Yehova?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Mawu a Mulungu Amakuthandizani Mokwanira?
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kusonkhana Pamodzi Kumatithandiza
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 May tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Yehova Akhoza Kukupatsani Zambiri Kuposa Pamenepa”

Amaziya analemba ganyu asilikali kuti amenyane ndi adani a Mulungu (2Mb 25:5, 6)

Munthu wa Mulungu analangiza Amaziya kuti asagwiritse ntchito asilikaliwo (2Mb 25:7, 8; it-1 1266 ¶6)

Yehova akanabwezera Amaziya zinthu zambiri zoposa ndalama zomwe anawononga (2Mb 25:9, 10)

Zithunzi: Mlongo wachitsikana akuganizira zinthu ziwiri zosiyana zimene angachite pa moyo. 1. Akucheza ndi nzake yemwe si wa Mboni pamene akupita m’kalasi; Ali mu utumiki ndi mlongo wachikulire. 2. Akugwira ntchito yolembedwa mpaka usiku; Akugwira nawo mosangalala ntchito yomanga malo olambirira. 3. Akufotokozera anzake zinthu zokhudza ntchito; Akuchititsa phunziro la Baibulo ndi mzimayi wina.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndingasiye zinthu ziti kuti ndizichita zambiri potumikira Yehova? Kodi ndi madalitso ati amene ndingapeze ngati nditachita zimenezi?’​—Mki 3:10; w21.08 30 ¶16.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena