Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 5
  • Kusamvera Kumapweteketsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kusamvera Kumapweteketsa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kutumikira Yehova Sikovuta Kwambiri
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzichita Chiyani?”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Baibulo Ndi Buku Limene Limanena Zoona
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kusamvera Kumapweteketsa

Aisiraeli ena anakwatirana ndi anthu amene ankalambira mafano (Eza 9:1, 2; w06 1/15 20 ¶1)

Iwo sanatsatire malamulo a Mulungu omwe anali omveka bwino (Eza 9:10-12)

Kusamvera kwawo kunabweretsa mavuto ambiri kwa iwowo komanso mabanja awo (Eza 10:10, 11, 44)

Mlongo yemwe anakwatiwa ndi mwamuna yemwe si Mboni ndipo tsopano ali ndi mwana, akukumbukira nthawi imene anali wolimba mwauzimu. Patebulo pali kambale koikamo phulusa la ndudu momwe muli zidutswa za ndudu. Mwamuna wake waledzera ndipo wagona pa mpando.

Lamulo lililonse limene Yehova amatipatsa, limakhala lotithandiza. (w09 10/1 10 ¶6) Kumvera kumatithandiza kuti tipewe mavuto ambiri panopa, komanso tidzapeza madalitso osatha m’tsogolo.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi kumvera Yehova kwandithandiza bwanji kuti ndipewe mavuto?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena