Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 12
  • Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kupereka Nsembe Zokondweretsa Mulungu
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Kodi Mungapereke Chiyani pa Ntchito ya Ufumu?
    Nsanja ya Olonda—2013
  • “Ine Ndilipo! Nditumizeni”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Anthu Okhulupirika kwa Yehova Amakwaniritsa Zimene Alonjeza
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 12

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova

Mabanja anapemphedwa kuti asiye nyumba komanso malo awo n’kupita ku Yerusalemu (Ne 11:1; w98 10/15 22 ¶13)

Anthu omwe anasiya zinthu zimenezi anadalitsidwa (Ne 11:2; w86 2/15 31)

Nthawi zonse madalitso ochokera kwa Yehova amakhala ochuluka kwambiri kuposa zinthu zimene tingasiye (Mki 3:10; w16.04 8 ¶15)

Zithunzi: 1. Banja likulongedza katundu wawo m’makatoni ndi m’chikwama. 2. Banja lomwe lija, lomwe likutumikira m’dziko lina, likulalikira mzimayi.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndapeza madalitso otani chifukwa cha zinthu zomwe ndinasiya pofuna kutumikira Yehova?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena