Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsamba 5
  • “Ine Ndilipo! Nditumizeni”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Ine Ndilipo! Nditumizeni”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Anasiya Zinthu Zina Chifukwa cha Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Mungapereke Chiyani pa Ntchito ya Ufumu?
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Mukhale ndi Zolinga mu Chaka Chautumiki Chikubwerachi​—Samukirani Kumene Kukufunika Olalikira Ufumu Ambiri
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Kodi Mungatumikire ku Gawo Losoŵa Kwambiri?
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2001
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 December tsamba 5

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

“Ine Ndilipo! Nditumizeni”

Banja la a Williams likukonzekera ndipo kenako likusamukira kudziko lina

Tonsefe tiyenera kutsanzira Yesaya pokhala ndi mtima wodzipereka. Iye anasonyeza chikhulupiriro ndipo anavomera mwamsanga kutumidwa ngakhale kuti sankadziwa zambiri zokhudza ntchito imene agwire. (Yes. 6:8) Kodi inuyo mungasinthe zinthu zina pa moyo wanu kuti mukatumikire kudera limene kukufunika olalikira Ufumu ambiri? (Sal. 110:3) N’zoona kuti muyenera “kuwerengera” mtengo wake musanasankhe kusamuka. (Luka 14:27, 28) Komabe ndi bwino kukhala ofunitsitsa kusiya zinthu zina kuti muwonjezere zimene mumachita pa ntchito yolalikira. (Mat. 8:20; Maliko 10:28-30) Vidiyo yakuti Kusamukira Kumene Kukufunika Olalikira Ambiri, imasonyeza kuti madalitso amene timapeza potumikira Yehova amakhala ambiri kuposa zinthu zimene tingasiye.

MUKAONERA VIDIYOYI, YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Kodi anthu a m’banja la a Williams analolera kusiya komanso kusintha zinthu ziti kuti akatumikire ku Ecuador?

  • Kodi anaganizira zinthu ziti posankha dziko loti akatumikire?

  • Kodi anapeza madalitso otani?

  • Kodi mungapeze kuti mfundo zokuthandizani ngati mukufuna kusamukira kudera limene kukufunika ofalitsa ambiri?

PA KULAMBIRA KWANU KWA PABANJA, KAMBIRANANI MAFUNSO AWA:

  • Kodi banja lathu lingawonjezere bwanji zimene timachita potumikira Yehova? (km 8/11 4-6)

  • Ngati sitingathe kusamukira kudera lina, kodi tingawonjezere bwanji zimene timachita pothandiza mpingo wathu? (w16.03 23-25)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena