Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • yb17 tsamba 177-192
  • Ziwerengero Zonse za 2016

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ziwerengero Zonse za 2016
  • Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017
  • Nkhani Yofanana
  • Ziwerengero Zonse za 2015
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2016
  • Ziwerengero Zonse za 2017
    Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2017 la Mboni za Yehova
  • Ziwerengero Zonse za 2013
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova 2014
  • Ziwerengero Zonse za 2014
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2015
Onani Zambiri
Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017
yb17 tsamba 177-192

Ziwerengero Zonse za 2016

  • Nthambi za Mboni za Yehova: 89

  • Mayiko Amene Anatumiza Lipoti:  240

  • Mipingo Yonse: 119,485

  • Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 20,085,142

  • Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 18,013

  • Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira: 8,340,847

  • Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 8,132,358

  • Maperesenti a Mmene Ofalitsa Anawonjezekera Poyerekeza ndi 2015: 1.8

  • Obatizidwa Onse: 264,535

  • Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 459,393

  • Avereji ya Apainiya Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,157,017

  • Maola Onse Amene Tinathera mu Utumiki: 1,983,763,754

  • Avereji ya Maphunziro a Baibulo Mwezi Uliwonse: 10,115,264

M’chaka cha utumiki cha 2016, Mboni za Yehova zinagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola 213 miliyoni a ku America posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira dera pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 19,818 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’Gulu Lapadziko Lonse la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena