Ziwerengero Zonse za 2015
Nthambi za Mboni za Yehova: 89
Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 240
Mipingo Yonse: 118,016
Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 19,862,783
Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 15,177
Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira: 8,220,105
Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 7,987,279
Maperesenti a Mmene Ofalitsa Anawonjezekera Poyerekeza ndi 2014: 1.5
Obatizidwa Onse: 260,273
Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 443,504
Avereji ya Apainiya Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,135,210
Maola Onse Amene Tinathera mu Utumiki: 1,933,473,727
Avereji ya Maphunziro a Baibulo Mwezi Uliwonse: 9,708,968
M’chaka cha utumiki cha 2015, Mboni za Yehova zinagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola 236 miliyoni posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira dera pa utumiki wawo. Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 26,011 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’Gulu Lapadziko Lonse la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.