Nthambi za Mboni za Yehova: 96
Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 239
Mipingo Yonse: 111,719
Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 19,013,343
Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 12,604
Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira: 7,782,346
Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 7,538,994
Maperesenti a Mmene Ofalitsa Anawonjezekera Poyerekeza ndi 2011: 1.9
Obatizidwa Onse: 268,777
Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 416,993
Avereji ya Apainiya Okhazikika Mwezi Uliwonse: 950,022
Maola Onse Amene Tinathera mu Utumiki: 1,748,697,447
Avereji ya Maphunziro a Baibulo Mwezi Uliwonse: 8,759,988
M’chaka chautumiki cha 2012, Mboni za Yehova zinagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola 184 miliyoni posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira oyendayenda pamene anali kuchita utumiki wawo.
◼ Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 21,612 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’Gulu Lapadziko Lonse la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.