Ziwerengero Zonse za 2013
Nthambi za Mboni za Yehova: 91
Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 239
Mipingo Yonse: 113,823
Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 19,241,252
Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 13,204
Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikira: 7,965,954
Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 7,698,377
Maperesenti a Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2012: 2.1
Obatizidwa Onse: 277,344
Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 496,089
Avereji ya Apainiya Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,025,677
Maola Onse Amene Tinalalikira: 1,841,180,235
Avereji ya Maphunziro a Baibulo Mwezi Uliwonse: 9,254,963
M’chaka chautumiki cha 2013, Mboni za Yehova zinagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola 200 miliyoni posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira oyendayenda pamene anali kuchita utumiki wawo.
Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 22,719 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’Gulu Lapadziko lonse la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.