Ziwerengero Zonse za 2014
Nthambi za Mboni za Yehova: 90
Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 239
Mipingo Yonse: 115,416
Opezeka pa Chikumbutso: 19,950,019
Amene Anadya Zizindikiro: 14,121
Chiwerengero Chapamwamba cha Ofalitsa Ufumu: 8,201,545
Avereji ya Ofalitsa Amene Analalikira Mwezi Uliwonse: 7,867,958
Peresenti ya Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2013: 2.2
Obatizidwa Onse: 275,581
Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 635,298
Avereji ya Apainiya Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,089,446
Maola Onse Amene Tinalalikira: 1,945,487,604
Avereji ya Maphunziro a Baibulo Mwezi Uliwonse: 9,499,933
M’chaka chautumiki cha 2014, a Mboni za Yehova anagwiritsa ntchito ndalama zoposa madola 224 miliyoni posamalira apainiya apadera, amishonale ndi oyang’anira oyendayenda. Padziko lonse pali abale ndi alongo okwana 24,711 amene akutumikira m’maofesi a nthambi. Onsewa ali m’gulu la Atumiki Apadera a Nthawi Zonse a Mboni za Yehova.