Numeri 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo pa tsiku la zipatso zoyamba kucha,+ pamene muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova,+ paphwando lanu la masabata, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa pa tsikuli.+
26 Ndipo pa tsiku la zipatso zoyamba kucha,+ pamene muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova,+ paphwando lanu la masabata, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa pa tsikuli.+