40 Mʼchaka cha 25 kuchokera pamene tinatengedwa kupita ku ukapolo,+ kuchiyambi kwa chakacho, pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, mʼchaka cha 14 pambuyo poti mzinda wawonongedwa,+ pa tsiku limeneli mphamvu za Yehova zinayamba kugwira ntchito pa ine, ndipo iye ananditenga nʼkupita nane kumzinda.+