Ekisodo 40:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatero anatchinga mpanda+ kuzungulira bwalo la chihema chopatulika ndi guwa lansembe, ndipo anakoloweka nsalu yotchinga pachipata cha bwalolo.+ Chotero Mose anamaliza ntchitoyo.
33 Atatero anatchinga mpanda+ kuzungulira bwalo la chihema chopatulika ndi guwa lansembe, ndipo anakoloweka nsalu yotchinga pachipata cha bwalolo.+ Chotero Mose anamaliza ntchitoyo.