Yobu 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma palibe wanena kuti, ‘Kodi Mulungu, Wondipanga Wamkulu,+ ali kuti,Amene amapatsa anthu nyimbo usiku?’+
10 Koma palibe wanena kuti, ‘Kodi Mulungu, Wondipanga Wamkulu,+ ali kuti,Amene amapatsa anthu nyimbo usiku?’+