Yesaya 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu.
19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu.