Danieli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’chaka choyamba cha ulamuliro wa Belisazara+ mfumu ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Pa nthawi imeneyo, analemba zimene analotazo,+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:1 Ulosi wa Danieli, tsa. 129 Nsanja ya Olonda,10/1/1986, ptsa. 4, 6
7 M’chaka choyamba cha ulamuliro wa Belisazara+ mfumu ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Pa nthawi imeneyo, analemba zimene analotazo,+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo.