17 Zidzakhala choncho chifukwa chiwawa chimene unachitira Lebanoni+ chidzafika pa iwe ndiponso chifukwa cha kuwononga kwako kwakukulu kumene unaopseza nako zilombo zakutchire, kukhetsa magazi a anthu ndi chiwawa chimene unachitira dziko lapansi,+ tauni ndi onse okhala mmenemo.+