Aroma 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho abale anga, thupi la Khristu linakupangani kukhala akufa ku Chilamulo,+ kuti mukhale a winawake,+ a iye amene anaukitsidwa kwa akufa,+ kuti tibale zipatso+ kwa Mulungu.
4 Choncho abale anga, thupi la Khristu linakupangani kukhala akufa ku Chilamulo,+ kuti mukhale a winawake,+ a iye amene anaukitsidwa kwa akufa,+ kuti tibale zipatso+ kwa Mulungu.