Salimo 45:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwe mwana wanga wamkazi, mvetsera ndipo ona ndi kutchera khutu.Uiwale anthu ako ndi nyumba ya bambo ako.+ 2 Akorinto 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikukuchitirani nsanje,+ ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati+ ndi mwamuna mmodzi,+ Khristu,+ ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera+ kwa iye.
10 Iwe mwana wanga wamkazi, mvetsera ndipo ona ndi kutchera khutu.Uiwale anthu ako ndi nyumba ya bambo ako.+
2 Ndikukuchitirani nsanje,+ ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati+ ndi mwamuna mmodzi,+ Khristu,+ ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera+ kwa iye.