Aroma 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:30 Nsanja ya Olonda,2/15/1995, ptsa. 3, 7
30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+