Yakobo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Abale anga, pasakhale aphunzitsi ambiri pakati panu,+ podziwa kuti tidzalandira chiweruzo chachikulu.+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 169/15/1995, tsa. 309/15/1989, ptsa. 12-14
3 Abale anga, pasakhale aphunzitsi ambiri pakati panu,+ podziwa kuti tidzalandira chiweruzo chachikulu.+