Yuda 1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Yuda, kapolo wa Yesu Khristu koma m’bale wake wa Yakobo,+ ndikulembera oitanidwa+ okondedwa ndi Mulungu Atate, amene ali naye pa ubwenzi,+ amenenso asungidwa+ kuti akhale ogwirizana ndi Yesu Khristu.
1 Ine Yuda, kapolo wa Yesu Khristu koma m’bale wake wa Yakobo,+ ndikulembera oitanidwa+ okondedwa ndi Mulungu Atate, amene ali naye pa ubwenzi,+ amenenso asungidwa+ kuti akhale ogwirizana ndi Yesu Khristu.