Mateyu 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine, ndipo palibe amene akum’dziwa bwino Mwana koma Atate+ okha, komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha+ ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+ 1 Yohane 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Komanso, munthu wosunga malamulo ake amakhalabe wogwirizana naye.+ Iyenso amakhala wogwirizana ndi munthuyo, ndipo chifukwa cha mzimu+ umene anatipatsa, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+
27 Atate wanga wapereka zinthu zonse kwa ine, ndipo palibe amene akum’dziwa bwino Mwana koma Atate+ okha, komanso palibe amene akuwadziwa bwino Atate koma Mwana yekha+ ndi aliyense amene Mwanayo wafuna kumuululira za Atatewo.+
24 Komanso, munthu wosunga malamulo ake amakhalabe wogwirizana naye.+ Iyenso amakhala wogwirizana ndi munthuyo, ndipo chifukwa cha mzimu+ umene anatipatsa, timadziwa kuti ndife ogwirizana naye.+