Aroma 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti chilamulo+ cha mzimu+ umene umapatsa moyo+ mwa Khristu Yesu chakumasulani+ ku chilamulo cha uchimo ndi cha imfa.+ Aroma 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe, inu mukutsatira za mzimu,+ osati za thupi, ngati mzimu wa Mulungu ukukhaladi mwa inu.+ Ngati wina alibe mzimu wa Khristu,+ ameneyu si wa Khristu.
2 Pakuti chilamulo+ cha mzimu+ umene umapatsa moyo+ mwa Khristu Yesu chakumasulani+ ku chilamulo cha uchimo ndi cha imfa.+
9 Komabe, inu mukutsatira za mzimu,+ osati za thupi, ngati mzimu wa Mulungu ukukhaladi mwa inu.+ Ngati wina alibe mzimu wa Khristu,+ ameneyu si wa Khristu.