Yohane 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khalani ogwirizana ndi ine, inenso ndikhala wogwirizana ndi inu.+ Nthambi singabale zipatso payokha, pokhapokha ngati ndi yolumikizikabe kumpesawo. Chimodzimodzi inunso, simungabale zipatso mukapanda kukhala olumikizika kwa ine.+ 1 Yohane 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma zimene inu munamva pa chiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamva pa chiyambi zikakhalabe mumtima mwanu, mudzakhalanso ogwirizana+ ndi Mwana ndi Atate.+
4 Khalani ogwirizana ndi ine, inenso ndikhala wogwirizana ndi inu.+ Nthambi singabale zipatso payokha, pokhapokha ngati ndi yolumikizikabe kumpesawo. Chimodzimodzi inunso, simungabale zipatso mukapanda kukhala olumikizika kwa ine.+
24 Koma zimene inu munamva pa chiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamva pa chiyambi zikakhalabe mumtima mwanu, mudzakhalanso ogwirizana+ ndi Mwana ndi Atate.+