-
Chivumbulutso 14:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndipo mngelo winanso anatuluka kuguwa lansembe. Iyeyu anali ndi ulamuliro pa moto.+ Anafuula kwa mngelo amene anali ndi chikwakwa chakuthwa uja ndi mawu okweza, akuti: “Tsitsa chikwakwa chako chakuthwacho umwete mpesa wa padziko lapansi,+ ndi kusonkhanitsa pamodzi masango a mphesa zake, chifukwa mphesa zakezo zapsa.”
-