Chivumbulutso 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mngelo woyamba+ anapita n’kukathira mbale yake padziko lapansi.+ Pamenepo mliri wa zilonda zopweteka ndi zonyeka+ unagwa pakati pa anthu amene anali ndi chizindikiro cha chilombo,+ amenenso anali kulambira chifaniziro chake.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 221-223
2 Mngelo woyamba+ anapita n’kukathira mbale yake padziko lapansi.+ Pamenepo mliri wa zilonda zopweteka ndi zonyeka+ unagwa pakati pa anthu amene anali ndi chizindikiro cha chilombo,+ amenenso anali kulambira chifaniziro chake.+