January Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya January 2017 Zitsanzo za Ulaliki January 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 24-28 Yehova Amasamalira Anthu Ake January 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 29-33 “Mfumu Idzalamulira Mwachilungamo” January 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 34-37 Hezekiya Anadalitsidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chake MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Inu Yehova, . . . Chikhulupiriro Changa Chili mwa Inu” January 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 38-42 Yehova Amapereka Mphamvu kwa Munthu Wotopa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tisamaiwale Kupempherera Akhristu Amene Akuzunzidwa January 30–February 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 43-46 Yehova Ndi Mulungu Yemwe Amalosera Zoona