Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 5
  • Khristu Ndi Chitsanzo Chathu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Khristu Ndi Chitsanzo Chathu
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Kristu Chitsanzo Chathu
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
  • Moyo wa Mpainiya
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Moyo wa Mpainiya
    Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 5

Nyimbo 5

Khristu Ndi Chitsanzo Chathu

Losindikizidwa

(Aroma 5:8)

1. Yehova Mulungu,

Anatikondadi,

Potipatsa Mwana’ke monga dipo.

Khristu anakhala

Mkate woti tidye,

Kuti tipeze moyo wosatha.

2. Khristuyo anati

Tipemphe Mulungu

Kuti dzina lake liyeretsedwe.

Tipemphe Ufumu,

Chifuniro chake,

Ndipo tipemphe chakudya chathu.

3. Cho’nadi cha Yesu

Chinamasula ’nthu

Amene anam’tsata ngati nkhosa.

Tizifesa mbewu

Za Ufumu wake.

Tikatero tipeza chimwemwe.

(Onaninso Mat. 6:9-11; Yoh. 3:16; 6:31-51; Aef. 5:2.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena